MkwasoUncategorized

IMFA YA LULE: MHRC ikudikirabe apolisi alankhulepo

Wolemba: Rose Chipumphula CHALIRA ndi Bartholomew BOAZ

Bungwe la Malawi Human Rights Commission (MHRC) lati likudikirabe apolisi kuti amange apolisi asanu ndi anayi (9) amene adatchulidwa kuti adatengapo mbali pa imfa ya a Buleya Lule, koma apolisi ati zotsatira za kafukufuku wa nkhaniyi adazitumiza kale ku ofesi ya mkulu woona za  milandu.

A Lule adafera m’manja mwa apolisi atangoonekera ku bwalo la milandu ku Lilongwe. Iwo adamangidwa ndi apolisi mu Febuluwale chaka chino powaganizira kuti adali mmodzi mwa anthu amene adasowetsa mnyamata wa chialubino Goodson Fanizo kwa Mfumu Yayikulu Chilikumwendo m’boma la Dedza.

Madotolo atapima thupi la a Lule adapeza kuti mkuluyu adafa  chifukwa chootchedwa ndi nyetsi ya magetsi. Koma chodabwitsa chidali choti atamwalira mkuluyu, apolisi sadauze msanga achibale ake ndipo adadikira kuti padutse tsiku limodzi.

Lule: Adafera m’manja mwa apolisi

Bungwe la MHRC lidachita  kafukufuku wa nkhaniyi ndipo mu lipoti lomwe lidatulutsa mu Meyi chaka chino lidapempha mkulu wa apolisi kuti afufuze apolisi amene adamanga a Lule; amene adawasunga ndi kumawafunsa mafunso; ndiponso kuti adali m’manja mwa yani kufikira pomwe adamwalira, kuti adziwe kuti adatengapo mbali yotani.

Ena mwa apolisi amene adatchulidwa mu lipotili adali  wogwirizira udindo wa Komishonala a Evalista Chisale – amene ndi mkazi wa mtetezi wa mtsogoleri wa dziko lino a Norman Chisale, mkulu wa chigawo chapakati Insipekitala Ronex Kapesa ndi Insipekitala Mervin Gama.

Bungwe la MHRC lidapereka kuti malire pa 5 Ogasiti chaka chino kuti kafukufukuyu akhale atachitika ndipo apolisiwa amangidwe akapezeka olakwa. Koma ngakhale padutsa miyezi iwiri palibe chimene chachitika.

Mkulu wolankhulira bungwe la MHRC a David Nungu anati kumbali yao ayesetsa koma pakali pano “mpira uli m’manja mwa apolisi kuti aliuze dziko kuti nkhaniyi ili pati.”

“[Apolisi] Akuyenera kutiuza kuti amene adatchulidwawo apanga nawo chiyani? Tikudikira kuti anthu amene adatchulidwa aja amangidwe. Tikufuna kuti chilungamo chiyende ngati madzi chifukwa adaphwanya ufulu wa munthu wokhala ndi moyo,” anatero a Nungu.

Koma mneneri wa apolisi a James Kadzadzera wati kafukufuku wokhudza apolisi amene ada-tchulidwa kuti akukhudzidwa ndi imfa ya a Lule adachitika ndi zotsatira zake zinakaperekedwa kwa mkulu woona za milandu (Director of Public Prosecutions).

“Mkulu woona milandu ndi yemwe ali ndi yankho la mmene nkhaniyi itakhalire ndipo akanena zonse zotsatira mtundu wa Malawi udzauzidwa choona. Iyi ndi nthawi yomwe chilungamo chitadzadziwike. Padakali pano zonse zokhudza nkhaniyi zidatha ndipo nafe tikudikira omwe adalandira mafailo okhudza nkhaniyi kuti apange chiganizo, ” anatero a Kadadzera.

Mkwaso unalephera kulankhula ndi mkulu woona milandu a Mary Kachale chifukwa lamya yao ya    m’manja imangoitana. 

Koma a Kadadzera apempha Amalawi kuti asatope kudikira chifukwa ati nkhani zofufuza  zimatenga nthawi kuti azimalize.

One thought on “IMFA YA LULE: MHRC ikudikirabe apolisi alankhulepo

  • Aduilt entertainment oklahoma cityElen birkin nudePictures off breast
    reduction surgery salisburyFreee xxx bit torret moviesLisaa alison hentaiVintage rolls royfe pictureFrree facial cumshoots mp3 videosFreee faat ass pusssy
    viedosAmateur video wife handjob husbandDisco curtis tanners is gayHott russian girls fuckingBlack cock inn mommaSuckk andd swallow cuum viedeo freeAnal com azer sexoAmateur
    shpe box picsBiig black dick cum asianTeeen longFreee erotic jailbait storiesRespect gay
    travelWorld sexx lesbianSlim womnen with huge titsElectrc handsfree cum shot movieMother son sex
    swallowsSpdrm receptacles torrentMo nique sexPregnan seex t videosEvaa tamargo
    nudeFreee amateur girlffriend nudeSleepiong mmom soon seex sampleBill murray and asianPicck up asan womman pornSecretary pantuhose videoAppple bottom jeasns websiteSexxy kitt sex picsReed wett pussyChat cpub free sexWhite teen blaqck cockAdvice maan sexualMy lasst fuckPusssy liccking movie
    samplePolish babees with bbig titsMositureizing fafial gelDick votale diaperErottica tangasMicbael husesey nudeBiig
    dick frist info rememberNude leather sandalTeeen amateur couple hhome videoSlapp happ sexArlingtpn nudee wijfe xxx hard sex indian Slaves takoes dilldo up his arseFunnny fmale teen monologuesHolly
    fucked 18Old menn slut loadPink ffree pussyBriana banks free ponstar galleriesUrine
    saample femdomSplit-tail nudesDvd review thee bopob tubeDiscountd lingerieErrotic teens storiesVoyyeur motheer
    in lawNaked theaterKiki bard breast lsSmoking asss rding cockArrab
    sex gilrts nudeAting jobs forr teensZwergen pornoFreee sexy nuce cheerleaderFreee
    interacial deepthrokat analFree video srxy womenDown load ppsp pornAdult modell leaa fosterBigg
    teen tits nudeContribution videro amatteur gratuiteFarinelli vintageHomevideos pornClip haatcher movie nude teriPiano adult lessonSki vacations
    for adultsFaace fuck sexial positio pictureBuxty chiks fucked hardLicking pussy wgile fuckedBreas cancdr aand sonogramGay dragonball picsHentai kamesn ultimateApril white
    teens blck cocksBrast sagging aftewr pregnancyWomen frontal nudeFrree european pussy videosSlut featAult educcation organisationLa
    blue giel xxxCute thick teen pornVintage supreme jacketNude gaay hoot menTeen gangbang and swallowUncut coick swissFernandda gar a castaneda
    nudeFreee nuude photks chicksHottestt model nakedCrstal mdth ggay menShekale goldVirginn opoen pussySexy horeny lesbianFreee upskirt vidLesbisn gymnast pporn siteNaaked
    celebraates of the 1950sBrreast augmentation implants plastic surrgery lady missNautica torne
    ssm tgpYoungporn tgpUglyy porn tgpArt perfect teenErrotic slkavehood byy christian abernathyArabhec
    xxxx moviesJamnie lunerr nude pictureBlack fuk blond
    galleriesFrree amteur squirtig vidsI fucked myy matess mumToms
    porn movieRoom ieas ffor teen girlsViedeos pornFisting kinky seex free video clipFree hot sexy sex videoAmituerr pussy
    picturesMen with hard oon cocksPics of nnaked menn inn tthe locker roomBlack blzck
    gaay movie only sexClitorris orgasm moviesShiny glammour sluts tgpGirl driknks juice from assHommade tit cumshotFree wife seducxes yoyng teenShhelf assSeexy mass
    effect picsLoccal lesbiwn teensCelebns nhde in playboyIndentifying vintage gi jooe vehiclesWife
    homje pornMan fucking blow-up doll picsPhoto of women withh biig clitorisM.d.
    Forte fcial clwanser iiBech tubers amteur teen spySwingers shivedrs australiaUglly
    bitcch blow jobFree milf offiche pornTeachr blowjob clipsCutt onn vaginal openingCompletly frdee
    sexujal petifriles listGay mes pantsSlow computer duee too pornBonedless turkey breast bake timeTeenn ggang bang sexConsensual strapping bottomsSquirt and porn and
    pussyMomss aand ons porn moviesSeth rogn virginityJordan moderl
    pornTeen double penetration mpegsTotally spies clover sexyMerkin sexMoney for those wuth breast cancerVintage demolition derbiesStarr wwars hsntai freeRaate
    oon teern pregnancyPatrick star ault tee shirtsFree fetish
    video communityBig teeen booy gelleriesSex thhai tripSeattle escor leaRocck
    bottom bar milwaukeeBigg breawst ikplants picturesNuude image rubher stampsSex shopp antigonishSeex lesbian twin incestEmmbrace
    of the vampie ilano nudeRent sex slaveVinttage boudoir dollsTotal packiage nude
    menWoodman fucks young girlVirrgin air sstuck onn tarmacTeens squirting partiesAsia massage kensingtonAsian explorations ordgon sponsorsExtreme gay sNaked suhrf boardingFree
    nake celeb vidsAss tteen jeansDiick cuum picturesHot caplri cavapli
    sexLargest natural latina titsXxxx many women onee manSexx clipps foor mobilKendra fuckingFuck amateursGirls iin leather tgpMy first sexx teacdher mpgAvaatar porn celebrityRene and kkia annd
    sapphic eroticaBuety girll iin commanhdo movie

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *