Uncategorized

Limbani wasokoloka ndi ‘Khalidwe’

Wolemba:

Edwin GAWANI

Mtolankhani Wapadera

atswiri wodziwika bwino pa nyimbo za chamba cha ‘Reggae’ Limbani Chibwana walengeza kuti akuyembekezeka kutulutsa chimbale chake chachitatu chomwe mutu wake ndi ‘Chisomo’ chaka cha mawa.

Chibwana: Nyimboyi ikudzudzula mchitidwe womaloda kale la month

Koma asanatulutse chimbalechi, iye waganiza zosokolotsa imodzi mwa nyimbo zili mu chimbalechi yotchedwa ‘Khalidwe’ kuti anthu ayilawe. Iye anafotokoza kuti nyimboyi wayijambula ku studiyo yake ya CL Touch komanso mothandizidwa ndi namandwa winanso pa maimbidwe Lulu ku studiyo yake ya Mathumela Records.

Malingana ndi Chibwana, nyimbo ya ‘Khalidwe’ ikukamba za mchitidwe wa anthu ambiri omwe amakonda kutsamira pa kale la munthu chikhalirecho munthuyo ali mu nyengo zina zatsopano.“Mwachitsanzo, ndikukamba za mwana wobadwa mu…

Subscribe to Mkwaso newspaper and read the whole story