MkwasoZa M'dziko Muno

Gulu likupindula ndi ng’ombe za mkaka

Wolemba:

Taona MKANDAWIRE

Mtolankhani Wapadera

Gulu la alimi la Bvumbwe Farmers Cooperative Society kuchokera kwa Bvumbwe m’boma la Thyolo likusimba lokoma ndi ulimi wa ng’ombe za mkaka.

Gululi lomwe linayamba mchaka cha 1973 ndipo nthawi imeneyo linkatchedwa kuti Bvumbwe Dairy Cooperative Group linayamba ndi ng’ombe khumi zokha basi zomwe linapatsidwa ndi boma.

Wina mwa katundu amene gululi likupanga

M’zaka zonsezi, gululi lakhala likugulitsa mkaka ku makampani a Malawi Milking Industry, Malawi Dairy Industry komanso Dairy board. Kufikira pano, gululi limapangano yogati chifukwa cha kudzimadzima kwa magetsi poopa kuti mkaka …

Subscribe to Mkwaso newspaper and read the whole story