MkwasoUncategorizedZa M'dziko Muno

Phungu wachilimika kumwetsa anthu madzi aukhondo

Wolemba:

Raphael LIKAKA

Mtolankhani Wapadera

Mdooko kuyeserera kujiga mjigo

Phungu wa dera la kumpoto kwa Bwanje m’boma la Ntcheu a Nancy Chaola Mdooko apempha anthu a m’dera lawo kuti asamalire chitukuko cha mijigo (14) yomwe akumbitsa pofuna kuti anthu adzimwa madzi aukhondo.

A Mdooko womwenso ndi wachiwiri kwa nduna ya za mtengatenga (transport) amayankhula izi mdera la mfumu yayikulu Masasa pa mwambo wopereka mijigo 14 yomwe iwo akumbitsa m’dera…

Subscribe to Mkwaso newspaper and read the whole story