MkwasoUncategorizedZa M'dziko Muno

Aphunzitsi, ophunzira asimba lokoma

Wolemba:
Raphael LIKAKA
Mtolankhani Wapadera

A Kwelepeta (a chiwiri kumanja) kupereka mphatso kwa ophunzira. (Chithunzi: Raphael Likaka)

Pofuna kulimbikitsa aphunzitsi komanso ophunzira mu sukulu za mdera la Zomba Malosa, phungu wa ku Nyumba ya Malamulo m’derali a Grace Kwelepeta anapereka mphoto kwa aphunzitsi omwe anakhonzetsa bwino mayeso a sitandade 8 m’mayeso a bungwe la Malawi National Examination Board (MANEB).

Poyankhula pa mwambowo womwe unachitikira pa sukulu Songani, a Kwelepeta anati anapanga chikonzerochi pofuna ku-bzala mbewu ya chilimbikitso kuti chaka cha mawa aphunzitsi adzathe kukhonzetsanso bwino mayeso.

Iwo anati ophunzira kuti achite bwino pa maphunziro awo, zonse zimayambira ndi upangiri wa aphunzitsi choncho ndibwino…

Subscribe to Mkwaso newspaper and read the whole story