Namondwe wotchedwa Chido akuwodira
Nthambi yoona za nyengo yati ikuyang’anira mwa chidwi namondwe wotchedwa Chido yemwe wabadwa pa nyanja yayikulu ya India.Nthambiyi yati namondweyu akuyembekezeka kugwa mdziko la Mozambique makamaka mu dera la Nacala usiku wa loweluka pa 14 Disembala. Iyo yati itsatira bwino kayendedwe ka namondweyu ndipo adzipereka zotsatira zake kwa Amalawi.