Khonsolo ya Balaka ivomereza pulojekiti yothandiza kuchepetsa njala
Komiti yayikulu ya boma la Balaka lachisanu inavomereza pulojekiti yothandizira kuchepetsa njala komanso kunyentchera yomwe bungwe la Save the Children
Read MoreKomiti yayikulu ya boma la Balaka lachisanu inavomereza pulojekiti yothandizira kuchepetsa njala komanso kunyentchera yomwe bungwe la Save the Children
Read MoreApolisi m’boma la Balaka apulumutsa gogo wina yemwe amafuna kuchitidwa chipongwe poganiziridwa kuti ‘akumanga’ mvula m’mudzi wa Manjanja mfumu yayikulu
Read MoreApolisi ku Mangochi amanga Abdul-Karim Saidi pa mlandu wothawitsa mtsikana wachichepere wa zaka 14 wa fomu 2 m’bomali. Mneneri wa
Read MoreTimu ya FCB Nyasa Big Bullets yawona msana wa njira mu mpikisano wa Castel Cup itagonja ndi Mzuzu City Hammers
Read MoreNthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi yalengeza kuti chiwerengero cha anthu omwe amwalira ndi namondwe wa Chido tsopano chafika pa
Read MoreUnduna wa Zamaphunziro walengeza za kuyimitsidwa kwa maphunziro a pulayimale ndi sekondale m’maboma omwe akuyembekezeka kukumana ndi chiopsezo cha Namondwe
Read MoreNthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi (DODMA) ikudziwitsa anthu onse kuti malipoti ochokera ku Nthambi Yoona Zanyengo, atsindika kuti Namondwe
Read MoreAnabwera atakonzeka, zida zonse zili potelopo, koma zidazi sizidali zokwanira kuthandizira asirikali aku Zomba kupambana nkhondo. Ndithudi timu ya Red
Read MoreNthambi yoona za nyengo yati ikuyang’anira mwa chidwi namondwe wotchedwa Chido yemwe wabadwa pa nyanja yayikulu ya India.Nthambiyi yati namondweyu
Read MoreKukhala chete kwa mabungwe a Public Affairs Committee (PAC), mabungwe amipingo ndi mabungwe omwe siaboma – Civil Society Organizations (CSOs)
Read More