Akaidi aphunzira ntchito za manja
Akaidiwa ndiomwe amakhala kuti atsala pang’ono kutuluka ku ndende ndipo amabwera ku malowa kutatsala miyezi isanu ndi umodzi kuti amalize chilango chawo. Iwo amabwera ku Nyumba ya ‘Mpumuloyi’ kuti aphunzire ntchito zosiyansiyana za manja zomwe zimakawathandizira akatuluka.